Oweruza 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma Yefita anawauza kuti: “Ineyo ndi anthu anga tinalimbana koopsa ndi ana a Amoni.+ Inu ndinakuitanani kuti mudzandithandize koma simunandipulumutse m’manja mwawo.
2 Koma Yefita anawauza kuti: “Ineyo ndi anthu anga tinalimbana koopsa ndi ana a Amoni.+ Inu ndinakuitanani kuti mudzandithandize koma simunandipulumutse m’manja mwawo.