-
Oweruza 12:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 ankamuuza kuti: “Nena kuti Shiboleti.” Koma iye ankanena kuti: “Siboleti,” chifukwa sankatha kutchula mawuwa molondola. Akatero ankamugwira nʼkumuphera powolokera Yorodano pomwepo. Anthu a ku Efuraimu amene anaphedwa pa nthawiyi anali okwana 42,000.
-