Oweruza 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 anali kumuuza kuti: “Nena kuti Shiboleti.”+ Koma iye anali kunena kuti: “Siboleti,” chifukwa sankatha kutchula mawuwa molondola. Akatero anali kumugwira ndi kumupha powolokera Yorodano pomwepo. Pa nthawi imeneyo panafa anthu 42,000 a ku Efuraimu.+
6 anali kumuuza kuti: “Nena kuti Shiboleti.”+ Koma iye anali kunena kuti: “Siboleti,” chifukwa sankatha kutchula mawuwa molondola. Akatero anali kumugwira ndi kumupha powolokera Yorodano pomwepo. Pa nthawi imeneyo panafa anthu 42,000 a ku Efuraimu.+