Miyambo 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova amanyansidwa ndi munthu aliyense wa mtima wonyada.+ Ngakhale anthu atagwirana manja, munthu sangapewe chilango.+ Miyambo 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Aliyense wokonda machimo akukonda kulimbana.+ Aliyense wotalikitsa khomo lake akufunafuna kuwonongedwa.+ Mlaliki 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mawu a m’kamwa mwa munthu wanzeru amakhala osangalatsa,+ koma milomo ya munthu wopusa imamuwononga.+
5 Yehova amanyansidwa ndi munthu aliyense wa mtima wonyada.+ Ngakhale anthu atagwirana manja, munthu sangapewe chilango.+
19 Aliyense wokonda machimo akukonda kulimbana.+ Aliyense wotalikitsa khomo lake akufunafuna kuwonongedwa.+
12 Mawu a m’kamwa mwa munthu wanzeru amakhala osangalatsa,+ koma milomo ya munthu wopusa imamuwononga.+