Oweruza 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Abidoni mwana wa Hilele wa ku Piratoni anamwalira, ndipo anaikidwa mʼmanda ku Piratoni, mʼdera la Efuraimu, mʼphiri la Aamaleki.+
15 Kenako Abidoni mwana wa Hilele wa ku Piratoni anamwalira, ndipo anaikidwa mʼmanda ku Piratoni, mʼdera la Efuraimu, mʼphiri la Aamaleki.+