Oweruza 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mʼmasiku amenewo mu Isiraeli munalibe mfumu.+ Ndipo pa nthawiyi fuko la Dani+ linkafuna malo oti likakhaleko, chifukwa linali lisanalandirebe cholowa pakati pa mafuko a Isiraeli.+
18 Mʼmasiku amenewo mu Isiraeli munalibe mfumu.+ Ndipo pa nthawiyi fuko la Dani+ linkafuna malo oti likakhaleko, chifukwa linali lisanalandirebe cholowa pakati pa mafuko a Isiraeli.+