-
Oweruza 19:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Pa tsiku la 4, anadzuka mʼmawa nʼkukonzeka kuti anyamuke, koma bambo a mtsikanayo anauza mkamwini wawoyo kuti: “Muyambe mwadya kaye kuti mupeze mphamvu, kenako mukhoza kunyamuka.”
-