Oweruza 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa tsiku lachinayi, atadzuka m’mawa kwambiri monga mwa nthawi zonse, anakonzeka kuti anyamuke, koma bambo a mtsikanayo anauza mkamwini wawoyo kuti: “Yambani mwadya kaye mkate,+ kenako mukhoza kupita.”
5 Pa tsiku lachinayi, atadzuka m’mawa kwambiri monga mwa nthawi zonse, anakonzeka kuti anyamuke, koma bambo a mtsikanayo anauza mkamwini wawoyo kuti: “Yambani mwadya kaye mkate,+ kenako mukhoza kupita.”