Oweruza 19:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zitatero, aliyense amene anaona zimenezo anati: “Zoterezi sizinachitikepo kapena kuoneka kuchokera pa tsiku limene Aisiraeli anachoka kudziko la Iguputo mpaka lero. Nkhani imeneyi muiganizire mofatsa, muikambirane+ ndipo mutiuze zochita.”
30 Zitatero, aliyense amene anaona zimenezo anati: “Zoterezi sizinachitikepo kapena kuoneka kuchokera pa tsiku limene Aisiraeli anachoka kudziko la Iguputo mpaka lero. Nkhani imeneyi muiganizire mofatsa, muikambirane+ ndipo mutiuze zochita.”