Oweruza 19:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zitatero, aliyense amene anaona zimenezo anati: “Zoterezi sizinachitikepo kapena kuonekapo kuchokera pa tsiku limene ana a Isiraeli anatuluka m’dziko la Iguputo mpaka lero. Iganizireni mofatsa nkhaniyi, munenepo maganizo+ anu ndipo tigwirizane.”
30 Zitatero, aliyense amene anaona zimenezo anati: “Zoterezi sizinachitikepo kapena kuonekapo kuchokera pa tsiku limene ana a Isiraeli anatuluka m’dziko la Iguputo mpaka lero. Iganizireni mofatsa nkhaniyi, munenepo maganizo+ anu ndipo tigwirizane.”