Oweruza 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano amuna a Isiraeli analumbira ku Mizipa+ kuti: “Aliyense wa ife sadzapereka mwana wake wamkazi kuti akwatiwe ndi mwamuna wa fuko la Benjamini.”+
21 Tsopano amuna a Isiraeli analumbira ku Mizipa+ kuti: “Aliyense wa ife sadzapereka mwana wake wamkazi kuti akwatiwe ndi mwamuna wa fuko la Benjamini.”+