Oweruza 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho, anthu a fuko la Benjaminiwo anabwerera ndipo anawapatsa akazi a ku Yabesi-giliyadi amene sanawaphe aja.+ Koma akaziwo anali osakwanira.
14 Choncho, anthu a fuko la Benjaminiwo anabwerera ndipo anawapatsa akazi a ku Yabesi-giliyadi amene sanawaphe aja.+ Koma akaziwo anali osakwanira.