Oweruza 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho, Abenjaminiwo anabwerera pa nthawiyo. Ndipo anawapatsa akazi amene anawasunga ndi moyo pakati pa akazi a ku Yabesi-giliyadi,+ koma sanawapezere akazi okwanira.+
14 Choncho, Abenjaminiwo anabwerera pa nthawiyo. Ndipo anawapatsa akazi amene anawasunga ndi moyo pakati pa akazi a ku Yabesi-giliyadi,+ koma sanawapezere akazi okwanira.+