1 Samueli 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pa ulendo wina, Eli anadalitsa Elikana ndi mkazi wake, ndipo anati: “Yehova akupatsenso mwana kudzera mwa mkaziyu kuti alowe mʼmalo mwa amene anaperekedwa kwa Yehova.”+ Kenako makolowo anabwerera kwawo.
20 Pa ulendo wina, Eli anadalitsa Elikana ndi mkazi wake, ndipo anati: “Yehova akupatsenso mwana kudzera mwa mkaziyu kuti alowe mʼmalo mwa amene anaperekedwa kwa Yehova.”+ Kenako makolowo anabwerera kwawo.