-
1 Samueli 28:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Mzimayiyo anali ndi mwana wa ngʼombe wonenepa mʼnyumba mwake. Choncho anamupha msangamsanga. Kenako anatenga ufa nʼkuukanda ndipo anaphika mkate wopanda zofufumitsa.
-