1 Samueli 28:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano mkaziyo anali ndi mwana wa ng’ombe wonenepa+ m’nyumba yake. Choncho anam’pereka nsembe msangamsanga,+ ndipo anatenga ufa n’kuukanda ndi kuphika mikate yopanda chofufumitsa.
24 Tsopano mkaziyo anali ndi mwana wa ng’ombe wonenepa+ m’nyumba yake. Choncho anam’pereka nsembe msangamsanga,+ ndipo anatenga ufa n’kuukanda ndi kuphika mikate yopanda chofufumitsa.