1 Samueli 29:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akisi anayankha Davide kuti: “Ineyo ndikuona kuti wakhala ukuchita zabwino ngati mngelo wa Mulungu.+ Koma akalonga a Afilisiti ndi amene anena kuti, ‘Musamulole kuti apite nafe kunkhondo.’
9 Akisi anayankha Davide kuti: “Ineyo ndikuona kuti wakhala ukuchita zabwino ngati mngelo wa Mulungu.+ Koma akalonga a Afilisiti ndi amene anena kuti, ‘Musamulole kuti apite nafe kunkhondo.’