1 Samueli 29:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Akisi anayankha Davide kuti: “Ndikudziwa bwino kuti wakhala ukundichitira zinthu zabwino, ngati mngelo wa Mulungu.+ Koma akalonga a Afilisiti ndi amene anena kuti, ‘Musalole kuti ameneyu apite nafe kunkhondo.’
9 Pamenepo Akisi anayankha Davide kuti: “Ndikudziwa bwino kuti wakhala ukundichitira zinthu zabwino, ngati mngelo wa Mulungu.+ Koma akalonga a Afilisiti ndi amene anena kuti, ‘Musalole kuti ameneyu apite nafe kunkhondo.’