Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 27:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Akisi anakhulupirira+ Davide, ndipo mumtima mwake anati: “Mosakayikira, Davide wakhala fungo lonunkha kwa anthu akwawo Aisiraeli,+ ndipo iye akhala mtumiki wanga mpaka kalekale.”

  • 2 Samueli 14:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 ine mtumiki wanu ndinaganiza kuti, ‘Mawu a mbuyanga mfumu andipatsa mpumulo.’ Pakuti inu mbuyanga mfumu muli ngati mngelo+ wa Mulungu woona, wokhoza kusiyanitsa chabwino ndi choipa.+ Ndipo Yehova Mulungu wanu akhale nanu.”

  • 2 Samueli 14:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Mtumiki wanu Yowabu wachita zimenezi kuti asinthe mmene mukuonera nkhaniyi. Koma inu mbuyanga muli ndi nzeru ngati mngelo+ wa Mulungu woona, moti mukudziwa zonse za padziko lapansi.”

  • 2 Samueli 19:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Choncho mtumiki wangayo anandinenera+ ine mtumiki wanu miseche kwa inu mbuyanga mfumu. Koma inu mbuyanga mfumu muli ngati mngelo+ wa Mulungu woona, motero chitani zimene zili zabwino kwa inu.

  • Miyambo 14:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Mfumu imasangalala ndi wantchito wochita zinthu mozindikira,+ koma imakwiya ndi wantchito wochita zinthu zochititsa manyazi.+

  • Agalatiya 4:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 inuyo simunanyansidwe ndi matenda anga, amene anali mayesero kwa inu, ndipo simunalavule malovu ponyansidwa nawo, koma munandilandira ngati mngelo+ wa Mulungu, ngati Khristu Yesu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena