2 Samueli 19:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Choncho mtumiki wangayo anandinenera+ ine mtumiki wanu miseche kwa inu mbuyanga mfumu. Koma inu mbuyanga mfumu muli ngati mngelo+ wa Mulungu woona, motero chitani zimene zili zabwino kwa inu.
27 Choncho mtumiki wangayo anandinenera+ ine mtumiki wanu miseche kwa inu mbuyanga mfumu. Koma inu mbuyanga mfumu muli ngati mngelo+ wa Mulungu woona, motero chitani zimene zili zabwino kwa inu.