1 Samueli 29:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Akisi anayankha Davide kuti: “Ndikudziwa bwino kuti wakhala ukundichitira zinthu zabwino, ngati mngelo wa Mulungu.+ Koma akalonga a Afilisiti ndi amene anena kuti, ‘Musalole kuti ameneyu apite nafe kunkhondo.’ 2 Samueli 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ine mtumiki wanu ndinaganiza kuti, ‘Mawu a mbuyanga mfumu andipatsa mpumulo.’ Pakuti inu mbuyanga mfumu muli ngati mngelo+ wa Mulungu woona, wokhoza kusiyanitsa chabwino ndi choipa.+ Ndipo Yehova Mulungu wanu akhale nanu.”
9 Pamenepo Akisi anayankha Davide kuti: “Ndikudziwa bwino kuti wakhala ukundichitira zinthu zabwino, ngati mngelo wa Mulungu.+ Koma akalonga a Afilisiti ndi amene anena kuti, ‘Musalole kuti ameneyu apite nafe kunkhondo.’
17 ine mtumiki wanu ndinaganiza kuti, ‘Mawu a mbuyanga mfumu andipatsa mpumulo.’ Pakuti inu mbuyanga mfumu muli ngati mngelo+ wa Mulungu woona, wokhoza kusiyanitsa chabwino ndi choipa.+ Ndipo Yehova Mulungu wanu akhale nanu.”