2 Samueli 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiye kuli bwanji pamene anthu oipa apha munthu wolungama pabedi mʼnyumba yake? Kodi sindiyenera kufuna magazi ake mʼmanja mwanu+ ndiponso kukuchotsani padzikoli?”
11 Ndiye kuli bwanji pamene anthu oipa apha munthu wolungama pabedi mʼnyumba yake? Kodi sindiyenera kufuna magazi ake mʼmanja mwanu+ ndiponso kukuchotsani padzikoli?”