2 Samueli 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Davide anagonjetsa Hadadezeri, mwana wa Rehobu mfumu ya Zoba,+ pamene Hadadezeriyo ankapita kumtsinje wa Firate+ kukabwezeretsa ulamuliro wake.
3 Davide anagonjetsa Hadadezeri, mwana wa Rehobu mfumu ya Zoba,+ pamene Hadadezeriyo ankapita kumtsinje wa Firate+ kukabwezeretsa ulamuliro wake.