2 Samueli 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Atatsala pangʼono kufika pamwala waukulu umene uli ku Gibiyoni,+ Amasa+ anabwera kudzakumana nawo. Yowabu anali atavala zovala zankhondo ndipo anaika lupanga mʼchimake nʼkulikoleka mʼchiuno mwake. Atayandikira Amasa, lupangalo linagwa.
8 Atatsala pangʼono kufika pamwala waukulu umene uli ku Gibiyoni,+ Amasa+ anabwera kudzakumana nawo. Yowabu anali atavala zovala zankhondo ndipo anaika lupanga mʼchimake nʼkulikoleka mʼchiuno mwake. Atayandikira Amasa, lupangalo linagwa.