-
2 Samueli 20:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Mnyamata wina wa Yowabu anaima pafupi ndi Amasa ndipo ankanena kuti: “Aliyense amene ali kumbali ya Yowabu komanso ya Davide, atsatire Yowabu!”
-