2 Samueli 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zitatero, mmodzi mwa anyamata a Yowabu anaimirira pafupi ndi Amasa ndipo anali kunena kuti: “Aliyense amene amagwirizana ndi Yowabu ndiponso aliyense wa Davide+ atsatire Yowabu!”
11 Zitatero, mmodzi mwa anyamata a Yowabu anaimirira pafupi ndi Amasa ndipo anali kunena kuti: “Aliyense amene amagwirizana ndi Yowabu ndiponso aliyense wa Davide+ atsatire Yowabu!”