-
2 Samueli 20:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Pa nthawiyi nʼkuti mtembo wa Amasa uli kwala pamagazi ake, pakati pa msewu. Mnyamata uja ataona kuti anthu onse akumaima pamalopo, anachotsa mtembo wa Amasa nʼkuuika patchire. Kenako anauphimba ndi chovala chifukwa anaona kuti aliyense akafika pamalowo, ankaima.
-