-
2 Samueli 20:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Choncho Yowabu anayandikira ndipo mayiyo anati: “Kodi ndinu a Yowabu?” Yowabu anayankha kuti: “Inde, ndine.” Ndiyeno mayiyo anati: “Tamverani zimene ine kapolo wanu ndikufuna kukuuzani.” Yowabu anayankha kuti: “Ndikumvetsera.”
-