2 Samueli 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho Yowabu anayandikira ndipo mkaziyo anati: “Kodi ndiwe Yowabu?” Pamenepo Yowabu anayankha kuti: “Inde, ndine.” Pamenepo mkaziyo anati: “Tamvera mawu a kapolo wako wamkazi.”+ Yowabu anayankha kuti: “Ndikumvetsera.”
17 Choncho Yowabu anayandikira ndipo mkaziyo anati: “Kodi ndiwe Yowabu?” Pamenepo Yowabu anayankha kuti: “Inde, ndine.” Pamenepo mkaziyo anati: “Tamvera mawu a kapolo wako wamkazi.”+ Yowabu anayankha kuti: “Ndikumvetsera.”