-
2 Samueli 20:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndiyeno mayiyo anati: “Kale anthu ankanena kuti, ‘Akafunsire nzeru kumzinda wa Abele,’ ndipo akatero nkhani inkathera pomwepo.
-