-
2 Samueli 20:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndiyeno mkaziyo ananena kuti: “Nthawi zakale aliyense anali kunena kuti, ‘Akafunsire nzeru ku Abele, ndipo adzapezadi njira yothetsera nkhani yake.’
-