-
1 Mafumu 8:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Inu Yehova Mulungu wanga, mumvetsere pemphero la mtumiki wanu ndi pempho lake lopempha chifundo. Imvani kulira kwanga kopempha thandizo komanso pemphero limene ine mtumiki wanu ndikupemphera kwa inu lero.
-