1 Mafumu 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mutembenukire ku pemphero+ la mtumiki wanu ndi pempho lake lopempha chifundo,+ inu Yehova Mulungu wanga. Mverani kulira kwanga kochonderera ndi pemphero limene ine mtumiki wanu ndikupemphera pamaso panu lero.+
28 Mutembenukire ku pemphero+ la mtumiki wanu ndi pempho lake lopempha chifundo,+ inu Yehova Mulungu wanga. Mverani kulira kwanga kochonderera ndi pemphero limene ine mtumiki wanu ndikupemphera pamaso panu lero.+