2 Mafumu 10:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho Yehova anauza Yehu kuti: “Chifukwa chakuti wachita bwino komanso wachita zoyenera kwa ine pochitira nyumba ya Ahabu+ zonse zimene zinali mumtima mwanga, ana ako aamuna adzakhala pampando wachifumu wa Isiraeli mpaka mʼbadwo wa 4.”+
30 Choncho Yehova anauza Yehu kuti: “Chifukwa chakuti wachita bwino komanso wachita zoyenera kwa ine pochitira nyumba ya Ahabu+ zonse zimene zinali mumtima mwanga, ana ako aamuna adzakhala pampando wachifumu wa Isiraeli mpaka mʼbadwo wa 4.”+