1 Mbiri 4:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Iwo anapha Aamaleki+ otsala omwe anathawa ndipo akukhala kumeneko mpaka lero.