Ekisodo 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Lemba zimenezi mʼbuku kuti anthu azidzazikumbukira ndipo umuuze Yoswa kuti, ‘Ndidzafafaniziratu Aamaleki padziko lapansi ndipo sadzakumbukiridwa nʼkomwe.’”+ Ekisodo 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ndipo anati: “Yehova adzamenya nkhondo ndi Aamaleki ku mibadwomibadwo+ chifukwa dzanja lawo laukira mpando wachifumu wa Ya.”+ 1 Samueli 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Sauli anapha Aamaleki+ kuyambira ku Havila+ mpaka ku Shura,+ pafupi ndi Iguputo.
14 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Lemba zimenezi mʼbuku kuti anthu azidzazikumbukira ndipo umuuze Yoswa kuti, ‘Ndidzafafaniziratu Aamaleki padziko lapansi ndipo sadzakumbukiridwa nʼkomwe.’”+
16 ndipo anati: “Yehova adzamenya nkhondo ndi Aamaleki ku mibadwomibadwo+ chifukwa dzanja lawo laukira mpando wachifumu wa Ya.”+