29 Pafupi ndi mbadwa za Manase panali Beti-seani+ ndi midzi yake yozungulira, Taanaki+ ndi midzi yake yozungulira, Megido+ ndi midzi yake yozungulira ndiponso Dori+ ndi midzi yake yozungulira. Mbadwa za Yosefe mwana wa Isiraeli zinkakhala mʼmizinda imeneyi.