1 Mbiri 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mtsogoleri wawo anali Ahiyezeri limodzi ndi Yowasi. Amenewa anali ana a Semaa wa ku Gibeya.+ Panalinso Yezieli ndi Peleti, ana a Azimaveti,+ Beraka, Yehu wa ku Anatoti
3 Mtsogoleri wawo anali Ahiyezeri limodzi ndi Yowasi. Amenewa anali ana a Semaa wa ku Gibeya.+ Panalinso Yezieli ndi Peleti, ana a Azimaveti,+ Beraka, Yehu wa ku Anatoti