1 Mbiri 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Panali Ahiyezeri mtsogoleri wawo ndiponso Yowasi. Amenewa anali ana a Semaa wa ku Gibeya.+ Panalinso Yezieli ndi Peleti, ana a Azimaveti,+ Beraka ndi Yehu wa ku Anatoti,+
3 Panali Ahiyezeri mtsogoleri wawo ndiponso Yowasi. Amenewa anali ana a Semaa wa ku Gibeya.+ Panalinso Yezieli ndi Peleti, ana a Azimaveti,+ Beraka ndi Yehu wa ku Anatoti,+