1 Mbiri 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ndiponso Isimaya wa ku Gibiyoni,+ mwamuna wamphamvu pa amuna 30+ komanso mtsogoleri wa amuna 30 amenewo. Panalinso Yeremiya, Yahazieli, Yohanani, Yozabadi wa ku Gedera,
4 ndiponso Isimaya wa ku Gibiyoni,+ mwamuna wamphamvu pa amuna 30+ komanso mtsogoleri wa amuna 30 amenewo. Panalinso Yeremiya, Yahazieli, Yohanani, Yozabadi wa ku Gedera,