1 Mbiri 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Isimaya wa ku Gibeoni,+ mwamuna wamphamvu pa amuna 30+ komanso mtsogoleri wa amuna 30 amenewo. Kenako panali Yeremiya, Yahazieli, Yohanani, Yozabadi wa ku Gedera,+
4 Isimaya wa ku Gibeoni,+ mwamuna wamphamvu pa amuna 30+ komanso mtsogoleri wa amuna 30 amenewo. Kenako panali Yeremiya, Yahazieli, Yohanani, Yozabadi wa ku Gedera,+