1 Mbiri 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma Davide anakwiya* chifukwa Yehova anakwiyira kwambiri Uza. Malo amenewa amadziwika ndi dzina lakuti Perezi-uza* mpaka lero. 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:11 Nsanja ya Olonda,10/1/2005, tsa. 11
11 Koma Davide anakwiya* chifukwa Yehova anakwiyira kwambiri Uza. Malo amenewa amadziwika ndi dzina lakuti Perezi-uza* mpaka lero.