1 Mbiri 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zitatero, Davide anakwiya+ chifukwa mkwiyo wa Yehova unaphulikira Uza modzidzimutsa. Chotero malo amenewo amatchedwa dzina lakuti Perezi-uza* kufikira lero. 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:11 Nsanja ya Olonda,10/1/2005, tsa. 11
11 Zitatero, Davide anakwiya+ chifukwa mkwiyo wa Yehova unaphulikira Uza modzidzimutsa. Chotero malo amenewo amatchedwa dzina lakuti Perezi-uza* kufikira lero.