2 Samueli 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zitatero, Davide anakwiya chifukwa mkwiyo wa Yehova unaphulikira Uza modzidzimutsa. Chotero malo amenewo amatchedwa dzina lakuti Perezi-uza* kufikira lero.+
8 Zitatero, Davide anakwiya chifukwa mkwiyo wa Yehova unaphulikira Uza modzidzimutsa. Chotero malo amenewo amatchedwa dzina lakuti Perezi-uza* kufikira lero.+