1 Mbiri 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zitatero, Davide anakwiya+ chifukwa mkwiyo wa Yehova unaphulikira Uza modzidzimutsa. Chotero malo amenewo amatchedwa dzina lakuti Perezi-uza* kufikira lero.
11 Zitatero, Davide anakwiya+ chifukwa mkwiyo wa Yehova unaphulikira Uza modzidzimutsa. Chotero malo amenewo amatchedwa dzina lakuti Perezi-uza* kufikira lero.