1 Mbiri 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno Davide anafunsiranso kwa Mulungu ndipo Mulungu woonayo anamuyankha kuti: “Usapite kukakumana nawo. Uwazembere kumbuyo nʼkuwaukira kutsogolo kwa zitsamba za baka.*+
14 Ndiyeno Davide anafunsiranso kwa Mulungu ndipo Mulungu woonayo anamuyankha kuti: “Usapite kukakumana nawo. Uwazembere kumbuyo nʼkuwaukira kutsogolo kwa zitsamba za baka.*+