1 Mbiri 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Davide anachitadi zimene Mulungu woona anamulamula,+ moti iwo anapha asilikali a Afilisiti kuchokera ku Gibiyoni mpaka ku Gezeri.+
16 Choncho Davide anachitadi zimene Mulungu woona anamulamula,+ moti iwo anapha asilikali a Afilisiti kuchokera ku Gibiyoni mpaka ku Gezeri.+