1 Mbiri 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Davide anachitadi monga mmene Mulungu woona anamulamulira,+ moti iwo anapha asilikali a Afilisiti kuchokera ku Gibeoni+ mpaka kukafika ku Gezeri.+
16 Choncho Davide anachitadi monga mmene Mulungu woona anamulamulira,+ moti iwo anapha asilikali a Afilisiti kuchokera ku Gibeoni+ mpaka kukafika ku Gezeri.+