Genesis 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo Nowa anachita zonse motsatira zimene Mulungu anamulamula. Anachitadi momwemo.+ Ekisodo 39:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Chotero ntchito yonse ya chihema chopatulika, kapena kuti chihema chokumanako, inatha, chifukwa ana a Isiraeli anachita zonse monga mmene Yehova analamulira Mose.+ Anachitadi momwemo. 1 Yohane 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+
32 Chotero ntchito yonse ya chihema chopatulika, kapena kuti chihema chokumanako, inatha, chifukwa ana a Isiraeli anachita zonse monga mmene Yehova analamulira Mose.+ Anachitadi momwemo.
3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+