-
1 Mbiri 19:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 akalonga a Aamoni anauza Hanuni kuti: “Kodi mukuganiza kuti Davide watumiza anthu odzakutonthozani chifukwa cholemekeza bambo anu? Kodi iye sanatumize atumiki akewa kuti adzafufuze zokhudza mzindawu nʼcholinga choti adzaulande?”
-